Cibvumbulutso 13:17 BL92

17 ndi kuti munthu sangakhoze kugula kapena kugulitsa, koma iye yekha wakukhala naco cilembo, ndilo dzina la cirombo, kapena ciwerengero ca dzina lace.

Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 13

Onani Cibvumbulutso 13:17 nkhani