Cibvumbulutso 15:1 BL92

1 Ndipo ndinaona cizindikilo cina m'mwamba, cacikuru ndi cozizwitsa, angelo asanu ndi awiri akukhala nayo miliri isanu ndi iwiri, ndiyo yotsiriza, kuti mwa iyo watsirizika mkwiyo wa Mulungu.

Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 15

Onani Cibvumbulutso 15:1 nkhani