4 Ndani adzakhala wosaopa ndi wosalemekeza dzina lanu Ambuye? Cifukwa Inu nokha muli woyera; cifukwa mitundu yonse idzadza nidzalambira pamaso panu, popeza zolungama zanu zidaonetsedwa.
Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 15
Onani Cibvumbulutso 15:4 nkhani