6 Ndipo anaturuka m'Kacisi angelo asanu ndi awiri akukhala nayo miliri isanu ndi iwiri, atabvala mwala woyera, ndi wonyezimira, namangira malamba agolidi pacifuwa pao,
Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 15
Onani Cibvumbulutso 15:6 nkhani