16 Ndipo nyanga khumi udaziona, ndi cirombo, izi zidzadana ndi mkazi wacigololoyo, nizidzamkhalitsa wabwinja wausiwa, nizidzadya nyama yace, nizidzampsereza ndi moto.
Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 17
Onani Cibvumbulutso 17:16 nkhani