1 Zitatha izi ndinaona mngelo wina wakutsika m'Mwamba wakukhala nao ulamuliro waukuru; ndipo dziko linaunikidwa ndi ulemerero wace.
Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 18
Onani Cibvumbulutso 18:1 nkhani