17 Ndipo ndinaona mngelo alikuima m'dzuwa; ndipo anapfuula ndi mau akuru alrunena 1 ndi mbalame zonse zakuuluka pakati pa mlengalenga: 2 Idzani kuno, sonkhanani ku phwando la Mulungu wamkuru,
Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 19
Onani Cibvumbulutso 19:17 nkhani