21 ndipo otsalawa anaphedwa ndi lupanga la iye wakukwera pa kavalo, ndilo lo turuka m'kamwa mwace; ndipo mbalame zonse zinakhuta ndi nyama zao.
Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 19
Onani Cibvumbulutso 19:21 nkhani