Cibvumbulutso 19:6 BL92

6 Ndipo ndinamva ngati mau a khamu lalikuru, ngati mkokomo wa madzi ambiri, ngati mau a mabingu olimba, nizinena, Aleluya; pakuti acita ufumu Ambuye Mulungu wathu, Wamphamvuyonse.

Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 19

Onani Cibvumbulutso 19:6 nkhani