Cibvumbulutso 2:1 BL92

1 Kwa mngelo wa Mpingo wa ku Efeso lemba;Izi azinena iye amene agwira nyenyezi zisanu ndi ziwiri m'dzanja lace lamanja, iye amene ayenda pakati pa zoikapo nyali zisanu ndi ziwiri zagolidi:

Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 2

Onani Cibvumbulutso 2:1 nkhani