Cibvumbulutso 2:11 BL92

11 Iye wokhala nalo khutu amve cimene Mzimu anena kwa Mipingo. Iye amene alakika sadzacitidwa coipa ndi imfa yaciwiri.

Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 2

Onani Cibvumbulutso 2:11 nkhani