Cibvumbulutso 2:13 BL92

13 Ndidziwa kumene ukhalako kuja kuli mpando wacifumu wa Satana; ndipo ugwira dzina langa, osakaniza cikhulupiriro canga, angakhale m'masiku a Antipa, mboni yanga, wokhulupirika wanga, amene anaphedwa pali inu, kuja akhalako Satana.

Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 2

Onani Cibvumbulutso 2:13 nkhani