Cibvumbulutso 2:16 BL92

16 Cifukwa cace lapa; ukapanda kutero ndidza kwa iwe posacedwa, ndipo ndidzacita nao nkhondo ndi lupanga la m'kamwa mwanga.

Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 2

Onani Cibvumbulutso 2:16 nkhani