Cibvumbulutso 2:18 BL92

18 Ndipo kwa mngelo wa Mpingo wa ku Tiyatira lemba:Izi azinena Mwana wa Mulungu, wakukhala nao maso ace ngati lawi la moto, ndi mapazi ace ngati mkuwa wonyezimira:

Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 2

Onani Cibvumbulutso 2:18 nkhani