Cibvumbulutso 2:24 BL92

24 Koma ndinena kwa inu, kwa otsala a ku Tiyatira, onse amene alibe ciphunzitso ici, amene sanazindikira zakuya za Satana, monga anena, Sindikusanjikizani katundu wina.

Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 2

Onani Cibvumbulutso 2:24 nkhani