Cibvumbulutso 20:11 BL92

11 Ndipo ndinaona, mpando wacifumu waukuru woyera, ndi iye wakukhalapo, amene dziko ndi m'mwamba zinathawa pamaso pace, ndipo sanapezedwamalo ao.

Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 20

Onani Cibvumbulutso 20:11 nkhani