Cibvumbulutso 20:3 BL92

3 namponya kuphompho, natsekapo, nasindikizapo cizindikilo pamwamba pace, kuti asanyengenso amitundu kufikira kudzatha zaka cikwi; patsogolo pace ayenera kumasulidwa iye kanthawi.

Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 20

Onani Cibvumbulutso 20:3 nkhani