Cibvumbulutso 21:13 BL92

13 kum'mawa zipata zitatu, ndi kumpoto zipata zitatu, ndi kumwela zipata zitatu, ndi kumadzulo zipata zitatu.

Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 21

Onani Cibvumbulutso 21:13 nkhani