Cibvumbulutso 21:16 BL92

16 Ndipo mzinda ukhala wampwamphwa; utali wace ulingana ndi kupingasa kwace: ndipo anayesa mzinda ndi bangolo, mastadiya zikwi khumi ndi ziwiri; utali wace, ndi kupingasa kwace, ndi kutalika kwace zilingana.

Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 21

Onani Cibvumbulutso 21:16 nkhani