1 Ndipo kwa mngelo wa Mpingo wa ku Sarde lemba:Izi anena iye wakukhala nayo mizimu isanu ndi iwiri ya Mulungu, ndi nyenyezi zisanu ndi riwiri: Ndidziwa nchito zako, kuti uli nalo dzina lakuti uli ndi moyo, ndipo uli wakufa.
Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 3
Onani Cibvumbulutso 3:1 nkhani