Cibvumbulutso 3:9 BL92

9 Taona, ndikupatsa ena oturuka m'sunagoge wa Satana akudzinenera okha ali Ayuda, osakhala Ayuda, komatu anama; taona, ndidzawadzetsa alambire pa mapazi ako, nazindikire kuti Ine ndakukonda.

Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 3

Onani Cibvumbulutso 3:9 nkhani