Cibvumbulutso 4:1 BL92

1 Zitatha izi ndinapenya, ndipo taonani, khomo lotseguka m'Mwamba, ndipo mau oyamba ndinawamva, ngati lipenga Iakulankhuia ndi ine, anati, Kwera kuno, ndipo ndidzakuonetsa zimene ziyenera kucitika m'tsogolomo.

Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 4

Onani Cibvumbulutso 4:1 nkhani