Cibvumbulutso 8:13 BL92

13 Ndipo ndinaona, ndipo ndinamva ciombankhanga cirikuuluka pakati pa mwamba, ndi kunena ndi mau akuru, Tsoka, tsoka, tsoka, iwo akukhala padz'ko, cifukwa ca mau otsala a lipenga la angelo atatu asanaombe.

Werengani mutu wathunthu Cibvumbulutso 8

Onani Cibvumbulutso 8:13 nkhani