Yohane 1:12 BL92

12 Koma onse amene anamlandira iye, kwa iwo anapatsa mphamvu yakukhala ana a Mulungu, kwa iwotu, akukhulupirira dzina lace;

Werengani mutu wathunthu Yohane 1

Onani Yohane 1:12 nkhani