11 Ine ndine Mbusa Wabwino; mbusa wabwino ataya moyo wace cifukwa ca nkhosa.
Werengani mutu wathunthu Yohane 10
Onani Yohane 10:11 nkhani