Yohane 10:25 BL92

25 Yesu anayankha iwo, Ndakuuzani, ndipo simukhulupirira, Nchitozi ndizicita Ine m'dzina la Atate wanga, zimenezi zindicitira umboni.

Werengani mutu wathunthu Yohane 10

Onani Yohane 10:25 nkhani