Yohane 10:33 BL92

33 Ayuda anamyankha iye, Cifukwa ca nchito yabwino sitikuponyani miyala, koma cifukwa ca mwano; ndi kuti Inu, muli munthu, mudziyesera nokha Mulungu,

Werengani mutu wathunthu Yohane 10

Onani Yohane 10:33 nkhani