19 koma ambiri a mwa Ayuda adadza kwa Marita ndi Mariya, kudzawatonthoza mtima pa mlongo wao.
Werengani mutu wathunthu Yohane 11
Onani Yohane 11:19 nkhani