Yohane 11:26 BL92

26 ndipo yense wakukhala ndi moyo, nakhulupirira Ine, sadzamwalira nthawi yonse. Kodi ukhulupirira ici?

Werengani mutu wathunthu Yohane 11

Onani Yohane 11:26 nkhani