Yohane 11:28 BL92

28 Ndipo m'mene anati ici anacoka naitana Mariya mbale wace m'tseri, ndi kuti, Wafika Mphunzitsi, akuitana iwe.

Werengani mutu wathunthu Yohane 11

Onani Yohane 11:28 nkhani