39 Yesu ananena, Cotsani mwala. Marita, mlongo wace wa womwalirayo, ananena ndi iye, Ambuye, adayamba kununkha: pakuti wagona masiku anai.
Werengani mutu wathunthu Yohane 11
Onani Yohane 11:39 nkhani