48 Ngati timleka iye kotero, onse adzakhulupirira iye; ndipo adzadza Aroma nadzacotsa malo athu ndi mtundu wathu.
Werengani mutu wathunthu Yohane 11
Onani Yohane 11:48 nkhani