9 Yesu anayankha, Kodi sikuli maora khumi ndi awiri usana? Ngati munthu ayenda usana sakhumudwa, cifukwa apenya kuunika kwa dziko lino lapansi,
Werengani mutu wathunthu Yohane 11
Onani Yohane 11:9 nkhani