Yohane 12:24 BL92

24 Indetu, indetu, ndinena ndi inu, Ngati mbeu ya tirigu siigwa m'nthaka, nifa, ikhala pa yokha iyo; koma ngati ifa, ibala cipatso cambiri.

Werengani mutu wathunthu Yohane 12

Onani Yohane 12:24 nkhani