27 Moyo wanga wabvutika tsopano; ndipo ndidzanena ciani? Atate, ndipulumutseni Ine ku nthawi iyi. Koma cifukwa ca ici ndinadzera nthawi iyi.
Werengani mutu wathunthu Yohane 12
Onani Yohane 12:27 nkhani