Yohane 12:29 BL92

29 Cifukwa cace khamu la anthu akuimirirako, ndi kuwamva ananena kuti kwagunda. Ena ananena, Mngelo walankhula ndi iye.

Werengani mutu wathunthu Yohane 12

Onani Yohane 12:29 nkhani