Yohane 12:36 BL92

36 2 Pokhala muli nako kuunika, khulupirirani kuunikako, kuti mukakhale ana a kuunikako.Izi Yesu analankhula, nacoka nawabisalira.

Werengani mutu wathunthu Yohane 12

Onani Yohane 12:36 nkhani