38 kuti mau a Yesaya mneneri akakwaniridwe, amene anati,3 Ambuye, wakhulupirira ndani kulalikira kwathu?Ndipo mkono wa Ambuye wabvumbulutsidwa kwa yani?
Werengani mutu wathunthu Yohane 12
Onani Yohane 12:38 nkhani