47 Ndipo ngati wina akumva mau anga, ndi kusawasunga, Ine sindimweruza; pakuti 11 sindinadza kudzaweruza dziko lapansi, koma kuti ndipulumutse dziko lapansi.
Werengani mutu wathunthu Yohane 12
Onani Yohane 12:47 nkhani