Yohane 12:50 BL92

50 Ndipo ndidziwa kuti lamulo lace liri moyo wosatha; cifukwa cace zimene ndilankhula, monga momwe Atate wanena ndi Ine, momwemo ndilankhula.

Werengani mutu wathunthu Yohane 12

Onani Yohane 12:50 nkhani