6 Koma ananena ici si cifukwa analikusamalira osauka, koma cifukwa anali mbala, ndipo pokhala nalo thumba, amabazoikidwamo.
Werengani mutu wathunthu Yohane 12
Onani Yohane 12:6 nkhani