Yohane 13:21 BL92

21 Yesu m'mene adanenaizi, anabvutika mumzimu, nacita umboni, nati, Indetu, indetu, ndinena ndi inu, kuti mmodzi wa inu adzandipereka Ine.

Werengani mutu wathunthu Yohane 13

Onani Yohane 13:21 nkhani