Yohane 13:29 BL92

29 Pakuti popeza Yudase anali nalo thumba, enaanalikuyesakuti Yesu ananena kwa iye, Gula zimene zitisowa paphwando; kapena, kuti apatse kanthu kwa aumphawi.

Werengani mutu wathunthu Yohane 13

Onani Yohane 13:29 nkhani