34 Ndikupatsani inu lamulo latsopano, kuti mukondane wina ndi mnzace; monga ndakonda Inu, kuti inunso mukondane wina ndi mnzace.
Werengani mutu wathunthu Yohane 13
Onani Yohane 13:34 nkhani