Yohane 13:38 BL92

38 Yesu anayankha, Moyo wako kodi udzautaya cifukwa ca Ine? Indetu, indetu, ndinena kwa iwe, Asanalire tambala udzandikana Ine katatu.

Werengani mutu wathunthu Yohane 13

Onani Yohane 13:38 nkhani