Yohane 14:2 BL92

2 M'nyumba ya Atate wanga alimo malo okhalamo ambiri. Ngati sikudali kutero, ndikadakuuzani inu; pakuti ndipita kukukonzerani inu malo.

Werengani mutu wathunthu Yohane 14

Onani Yohane 14:2 nkhani