Yohane 14:26 BL92

26 Koma 2 Nkhosweyo, Mzimu Woyera, amene Atate adzamtuma m'dzina langa, 3 Iyeyo adzaphunzitsa Inu zonse, nadzakumbutsa inu zinthu zonse zimene ndinanena kwa inu.

Werengani mutu wathunthu Yohane 14

Onani Yohane 14:26 nkhani