Yohane 14:28 BL92

28 Mwamva kuti Ine ndinanena kwa inu, 6 Ndimuka, ndipo ndidza kwa inu. Mukadandikonda Ine, mukadakondwera kuti ndipita kwa Atate; 7 pakuti Atate ali wamkuru ndi Ine.

Werengani mutu wathunthu Yohane 14

Onani Yohane 14:28 nkhani