Yohane 15:15 BL92

15 Sindichanso inu akapolo; cifukwa kapolo sadziwa cimene mbuye wace acita; koma ndacha inu abwenzi; cifukwa zonse zimene ndazimva kwa Atate wanga ndakudziwitsani.

Werengani mutu wathunthu Yohane 15

Onani Yohane 15:15 nkhani