Yohane 15:2 BL92

2 Nthambi iri yonse ya mwa Ine yosabala cipatso, aicotsa; ndi iri y'onse yakubala cipatso, aisadza, kuti ikabale cipatso cocuruka.

Werengani mutu wathunthu Yohane 15

Onani Yohane 15:2 nkhani